June 12-18
2 MBIRI 32-33
Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzilimbikitsa Abale ndi Alongo Anu Akakumana ndi Mavuto”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mb 33:15, 16—Kodi tingaphunzire chiyani pa chitsanzo cha Manase? (w21.10 4-5 ¶11-12)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 32:1-15 (th phunziro 11)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (4 min.) Kambiranani tsamba lomaliza la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo m’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo. (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 17)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 10 mfundo 5 (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Dzitetezeni kwa Anthu Ampatuko”: (10 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Zofunika Pampingo: (5 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 48 mfundo 1-4
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 90 ndi Pemphero