June 19-25
2 MBIRI 34-36
Nyimbo Na. 97 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mawu a Mulungu Amakuthandizani Mokwanira?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mb 35:20-23—Kodi ndi chenjezo lotani limene tikupeza pa zimene zinachitikira mfumu yabwino Yosiya? (w17.03 27 ¶15-17)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 35:1-14 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni kabuku ka Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, kenako kambiranani mwachidule mbali yakuti “Zimene Mungachite Kuti Muzipindula ndi Phunziro Lililonse.” (th phunziro 7)
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mudziwitseni za webusaiti yathu, ndipo musiyireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 11)
Nkhani: (5 min.) w17.09 25-26 ¶7-10—Mutu: Muzigwiritsa Ntchito Bwino Mawu a Mulungu pa Utumiki Wanu. (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Mukugwiritsa Ntchito Mokwanira Baibulo Longomvetsera?”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 48 mfundo 5, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 117 ndi Pemphero