Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Yosiya akung’amba chovala chake atamva buku la Chilamulo cha Yehova likuwerengedwa

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Mawu a Mulungu Amakuthandizani Mokwanira?

Kodi Mawu a Mulungu Amakuthandizani Mokwanira?

Yosiya anamvetsera mawu a Mulungu mosamala kwambiri (2Mb 34:18, 19; onani chithunzi chapachikuto)

Iye anayesetsa kuti amvetse bwino tanthauzo la zomwe anamva (2Mb 34:21; it-1 1157 ¶4)

Iye anachita zinthu mogwirizana ndi zomwe anaphunzira (2Mb 34:33; w09 6/15 10 ¶20)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndimatsatira mwamsanga zimene ndaphunzira zokhudza Yehova kuchokera m’Mawu ake Baibulo?’