June 26–July 2
EZARA 1-3
Nyimbo Na. 75 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzilola Kuti Yehova Azikugwiritsani Ntchito”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Eza 1:5, 6—Kodi tingaphunzire chiyani kuchokera kwa Aisiraeli ena amene anatsala ku Babulo? (w06 1/15 19 ¶1)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Eza 2:58-70 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 9)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 10 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Mumasangalala Mukamayambitsa Nkhani”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 49 mfundo 1-5
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero