Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzilola Kuti Yehova Azikugwiritsani Ntchito

Muzilola Kuti Yehova Azikugwiritsani Ntchito

[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Ezara.]

Yehova analimbikitsa mtima wa Mfumu Koresi kuti akamasule Aisiraeli (Eza 1:1-3; w22.03 14 ¶1)

Yehova analimbikitsa mtima wa anthu ake kuti akamangenso kachisi (Eza 1:5; w17.10 26 ¶2)

Ngati mungadzipereke, Yehova akhoza kuchititsa kuti mukhale chilichonse chimene iye akufuna kuti akwaniritse cholinga chake.