June 5-11
2 MBIRI 30-31
Nyimbo Na. 87 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kusonkhana Pamodzi Kumatithandiza”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mb 30:20—Kodi tingaphunzirepo chiyani kuchokera pa zimene Yehova anachita pomvetsera Hezekiya? (w18.09 6 ¶14-15)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 31:11-21 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (2 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 20)
Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku ka Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito phunziro 01. (th phunziro 18)
Nkhani: (5 min.) w19.01 11-12 ¶13-18—Mutu: Tizitamanda Yehova Poyankha Pamisonkhano. (th phunziro 16)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Khalani Bwenzi la Yehova—Uzikonzekera Zimene Ukayankhe: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’zotheka, funsani ana mafunso awa: Kodi mungakonzekere bwanji zoti mukayankhe pamisonkhano? N’chifukwa chiyani tiyenera kukhalabe osangalala ngakhale pamene sanatipatse mwayi woyankha?
Zimene Gulu Lathu Lachita: (10 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya June.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff kubwereza gawo 3
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 115 ndi Pemphero