May 1-7
2 MBIRI 17-19
Nyimbo Na. 114 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonera”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mb 17:9—Kodi tingaphunzirepo chiyani pa ntchito yophunzitsa imene Yehosafati anayambitsa? (w17.03 20 ¶10-11)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 17:1-19 (th phunziro 11)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya chitsanzo cha Ulendo Woyamba: Baibulo—Aro 15:4. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 18)
Nkhani: (5 min.) w21.05 17-18 ¶11-15—Mutu: Tizisangalalabe Ngakhale Pamene Anthu Sakufuna Kumvetsera. (th phunziro 16)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzidziona Mmene Yehova Amakuonerani”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 44 mfundo 5-6, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 111 ndi Pemphero