Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonera

Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonera

Mfumu Yehosafati inachita zinthu mopanda nzeru pamene inapanga mgwirizano ndi Mfumu Ahabu (2Mb 18:1-3; w17.03 24 ¶7)

Yehova anatumiza Yehu kuti akadzudzule Yehosafati (2Mb 19:1, 2)

Yehova anakumbukira zinthu zabwino zimene Yehosafati anachita (2Mb 19:3; w15 8/15 11-12 ¶8-9)

DZIFUNSENI KUTI, ‘M’malo momangoganizira zinthu zimene abale ndi alongo anga amalakwitsa, kodi ndimaona makhalidwe awo abwino ngati mmene Yehova amachitira?’