May 15-21
2 MBIRI 22-24
Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Amadalitsa Anthu Amene Amachita Zinthu Molimba Mtima”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mb 24:22—Kodi zimene Zekariya ananena mu ulosi wa palembali zinakwaniritsidwa bwanji? (it-2 1223 ¶13)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 22:1-12 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 17)
Nkhani: (5 min.) w10 2/15 6-8 ¶6-10—Mutu: Mzimu wa Yehova Udzakuthandizani Kukhala Olimba Mtima. (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 45 mfundo 4, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 37 ndi Pemphero