Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amadalitsa Anthu Amene Amachita Zinthu Molimba Mtima

Yehova Amadalitsa Anthu Amene Amachita Zinthu Molimba Mtima

Yehosabati ndi mwamuna wake Yehoyada anateteza Yehoasi kwa Ataliya (2Mb 22:11, 12; w09 4/1 24 ¶1-2)

Yehoyada anachita zinthu molimba mtima kuti aike Yehoasi kukhala mfumu (2Mb 23:1-11, 14, 15; w09 4/1 24 ¶3-5)

Yehoyada analandira ulemu wapadera pamene anaikidwa m’manda limodzi ndi mafumu (2Mb 24:15, 16; it-1 379 ¶5)

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi ndi mbali ziti zimene ndiyenera kusonyeza kuti ndine wolimba mtima pa utumiki wanga?