May 29–June 4
2 MBIRI 28-29
Nyimbo Na. 54 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mukhoza Kutumikira Yehova Ngakhale Makolo Anu Si Chitsanzo Chabwino”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mb 29:25—Kodi chitsanzo cha Natani chikutiphunzitsa chiyani pankhani ya ubwino wotsatira uphungu wochokera kwa Yehova? (w12 2/15 24-25)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 28:1-11 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 4)
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 19)
Phunziro la Baibulo: (6 min.) lff phunziro 10 mfundo 4 (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Yehova ndi ‘Tate wa Ana Amasiye’”: (8 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Zofunika Pampingo: (7 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 47
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 86 ndi Pemphero