Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mukhoza Kutumikira Yehova Ngakhale Makolo Anu Si Chitsanzo Chabwino

Mukhoza Kutumikira Yehova Ngakhale Makolo Anu Si Chitsanzo Chabwino

Mfumu Ahazi, yemwe anali bambo ake a Hezekiya, inachita zoipa zambiri (2Mb 28:1; w16.02 14 ¶8)

Hezekiya anasankha kutumikira Yehova ngakhale kuti bambo ake sanali chitsanzo chabwino (2Mb 29:1-3; w16.02 14 ¶9-11)

Hezekiya analimbikitsa ena kuti asasiye kutumikira Yehova chifukwa cha kusakhulupirika kwa bambo awo (2Mb 29:4-6)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingalimbikitse bwanji achinyamata amene makolo awo satumikira Yehova?’