May 8-14
2 MBIRI 20-21
Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Khulupirirani Yehova Mulungu Wanu”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mb 21:14, 15—Kodi ulosi wa Eliya wokhudza Yehoramu unakwaniritsidwa bwanji? (it-1 1271 ¶1-2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mb 20:20-30 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Wobwereza: Baibulo—Chv 21:3, 4. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 9)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 09 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Mwakonzeka Kukumana ndi Mavuto Azachuma?”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo. Ikambidwe ndi mkulu. Tchulaninso zilengezo zochokera ku ofesi ya nthambi kapena ku bungwe la akulu ngati zilipo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 45 mfundo 1-3
Mawu Omaliza (3 min.)