Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

June 10-16

MASALIMO 48-50

June 10-16

Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Makolo, Muzithandiza Banja Lanu Kudalira Kwambiri Gulu la Yehova

(10 min.)

Muzithandiza ana anu kuti azikonda kwambiri Yehova komanso gulu lake (Sl 48:12, 13; w22.03 22 ¶11; w11 3/15 19 ¶5-7)

Muziphunzitsa ana anu mbiri ya gulu lathu (w12 8/15 12 ¶5)

Muzikhala chitsanzo pophunzitsa ana anu kutsatira malangizo ochokera ku gulu la Yehova (Sl 48:14)

ZOMWE MUNGACHITE PA KULAMBIRA KWA PABANJA: Nthawi ndi nthawi muzionera ndi kukambirana mavidiyo opezeka pa gawo lakuti “Gulu Lathu” pa jw.org.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 49:6, 7​—Kodi Aisiraeli ankafunika kumakumbukira chiyani zokhudza chuma chimene anali nacho? (it-2 805)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Kulimba Mtima​—Zomwe Yesu Anachita

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 6 mfundo 1-2.

5. Kulimba Mtima​—Zomwe Mungachite Potsanzira Yesu

(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 6 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 73

6. Zofunika Pampingo

(15 min.)

7. Phunziro la Baibulo la Mpingo

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 103 ndi Pemphero