May 13-19
MASALIMO 38-39
Nyimbo Na. 125 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. Musamangokhalira Kudziimba Mlandu
(10 min.)
Kudziimba mlandu kwambiri kuli ngati kunyamula katundu wolemera kwambiri (Sl 38:3-8; w20.11 27 ¶12-13)
M’malo momangoganizira zimene munalakwitsa m’mbuyomu, muzikhala wofunitsitsa kuchita zomwe zingasangalatse Yehova (Sl 39:4, 5; w02 11/15 20 ¶1-2)
Ngakhale mukuona kuti n’zovuta kupemphera chifukwa choti mukudziimba mlandu, muzipempherabe (Sl 39:12; w21.10 15 ¶4)
Ngati mukudziimba mlandu kwambiri, muzikumbukira kuti Yehova ‘amakhululukira ndi mtima wonse’ anthu ochimwa omwe alapa.—Yes 55:7.
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Sl 39:1—Kodi ndi pa nthawi iti pamene tingagwiritse ntchito mfundo yakuti “ndidzaphimba pakamwa panga kuti ndisalankhule”? (w22.09 13 ¶16)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Sl 38:1-22 (th phunziro 2)
4. Kulankhula Mwaluso—Zomwe Paulo Anachita
(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 5 mfundo 1-2.
5. Kulankhula Mwaluso—Zomwe Mungachite Potsanzira Paulo
(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 5 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”
Nyimbo Na. 44
6. Zofunika Pampingo
(15 min.)
7. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 9 ¶17-24, bokosi patsamba 73