November 21-27
MLALIKI 7-12
Nyimbo Na. 41 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kumbukira Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”: (10 min.)
Mlal. 12:1—Achinyamata ayenera kugwiritsa ntchito nthawi ndi mphamvu zawo potumikira Mulungu (w14 1/15 18 ndime 3; w14 1/15 22 ndime 1)
Mlal. 12:2-7—Achinyamata angachite zambiri chifukwa sakhala ndi mavuto amene anthu okalamba amakumana nawo (w08 11/15 23 ndime 2; w06 11/1 16 ndime 9)
Mlal. 12:13, 14—Kutumikira Yehova n’kumene kungakuthandizeni kukhala osangalala (w11 11/1 21 ndime 1-6)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Mlal. 10:1—Kodi “uchitsiru pang’ono” ungawononge bwanji mbiri ya munthu? (w06 11/1 16 ndime 5)
Mlal. 11:1—Kodi ‘kutumiza mkate wako pamadzi’ kumatanthauza chiyani? (w06 11/1 16 ndime 7)
Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mlal. 10:12-20; 11:1-10
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) 2 Tim. 3:1-5—Kuphunzitsa Choonadi.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yes. 44:27-28; 45:1-2—Kuphunzitsa Choonadi.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 26 ndime 18-20—Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 95
“Achinyamata Musachedwe Kulowa ‘Pakhomo Lalikulu’”: (15 min.) Onetsani vidiyo yakuti Achinyamata—Yehova Amakukondani Kwambiri. (Imapezeka pa tv.pr418.com/ny pamene palembedwa kuti MISONKHANO NDI UTUMIKI WATHU.) Kenako kambiranani nkhaniyi.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 11 ndime 12-20 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 98.
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 148 ndi Pemphero
Kumbukirani: Muyenera kuika nyimboyi kuti onse amvetsere, kenako muibwerezenso kuti onse aimbe nawo.