Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

November 28–December 4

NYIMBO YA SOLOMO 1-8

November 28–December 4
  • Nyimbo Na. 106 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) bhs—Gwiritsani ntchito vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? kuti mugawire bukuli. (Dziwani izi: Musaonetse vidiyoyi m’chitsanzochi.)

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) bhs—Muitanireni munthuyo kumisonkhano.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 31-32 ndime 8-9

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 115

  • “Zimene Achinyamata Amadzifunsa—Kodi Ndafika Poti N’kukhala ndi Chibwenzi?”: (9 min.) Nkhani yochokera mu nkhani yakuti, “Zimene Achinyamata Amadzifunsa—Kodi Ndafika Poti N’kukhala ndi Chibwenzi?

  • Kodi Ndi Chikondi Chenicheni Kapena Kungotengeka Maganizo?: (6 min.) Onetsani ndiponso kukambirana vidiyo yakuti Kodi Ndi Chikondi Chenicheni Kapena Kungotengeka Maganizo?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 12 ndime 1-12

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 34 ndi Pemphero