November 7-13
MIYAMBO 27-31
Nyimbo Na. 86 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Baibulo Limafotokoza Zimene Mkazi Wabwino Amachita”: (10 min.)
Miy. 31:10-12—Amakhala wodalirika (w15 1/15 20 ndime 10; w00 2/1 31 ndime 2; it-2-E 1183)
Miy. 31:13-27—Amakhala wakhama ndiponso wanzeru (w00 2/1 31 ndime 3-4)
Miy. 31:28-31—Amakonda Yehova ndipo anthu amamulemekeza (w15 1/15 20 ndime 8; w00 2/1 31 ndime 5, 8)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Miy. 27:12—Kodi tingakhale bwanji ochenjera pa nkhani yosankha zosangalatsa? (w15 7/1 8 ndime 3)
Miy. 27:21—Kodi munthu angayesedwe bwanji ndi “chitamando” chimene walandira? (w11 8/1 29 ndime 1; w06 9/15 19 ndime 12)
Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Miy. 29:11-27; 30:1-4
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pambuyo poonetsa vidiyo iliyonse ya chitsanzo cha ulaliki, kambiranani mfundo zimene tikuphunzirapo. Limbikitsani ofalitsa kuti azilemba ulaliki wawowawo.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 89
“Mwamuna Wake Amadziwika Pazipata”: (5 min.) Nkhani yokambidwa ndi mkulu.
Zofunika Pampingo: (10 min.) Mukhozanso kukambirana mfundo zimene tikuphunzira mu Buku Lapachaka. (yb16 40-41)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 10 ndime 12-21 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 91
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 108 ndi Pemphero