Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 YOHANE 1-5

Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za M’dziko

Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za M’dziko

2:15-17

Satana amagwiritsa ntchito zinthu zitatu zotsatirazi zomwe dziko limalimbikitsa pofuna kutichititsa kuti tisiye kutumikira Yehova. Kodi zinthu zimenezi mungazifotokoze bwanji?

  • “Chilakolako cha thupi”

  • “Chilakolako cha maso”

  • “Kudzionetsera ndi zimene munthu ali nazo”