Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zimene Tinganene

Zimene Tinganene

●○○ ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi Mulungu anali ndi cholinga chotani potilenga?

Lemba: Gen. 1:27, 28

Funso la Ulendo Wotsatira: N’chifukwa chiyani tiyenera kukhulupirira kuti Mulungu adzakwaniritsa cholinga chake?

○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA

Funso: N’chifukwa chiyani tiyenera kukhulupirira kuti Mulungu adzakwaniritsa cholinga chake?

Lemba: Yos. 21:45

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Mulungu watilonjeza chiyani m’tsogolomu?

○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI

Funso: Kodi Mulungu watilonjeza chiyani m’tsogolomu?

Lemba: Chiv. 21:4

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tingatani kuti tidzalandire nawo madalitso amene Mulungu walonjeza?