Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

November 16-22

LEVITIKO 4-5

November 16-22

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Muzipereka kwa Yehova Zonse Zimene Mungathe”: (10 min.)

    • Le 5:5, 6​—Anthu amene anachita machimo ena ankafunika kupereka nsembe za kupalamula zimene zinali za nkhosa kapena mbuzi (it-2 527 ¶9)

    • Le 5:7​—Anthu osauka amene sakanatha kupereka nkhosa kapena mbuzi ankatha kupereka njiwa ziwiri kapena nkhunda ziwiri (w09 6/1 26 ¶3)

    • Le 5:11​—Anthu osauka amene sakanatha kupereka njiwa kapena nkhunda ankatha kupereka ufa wosalala wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa (w09 6/1 26 ¶4)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 5:1​—Kodi lemba limeneli lingathandize bwanji Akhristu? (w16.02 29 ¶14)

    • Le 5:15, 16​—Kodi zikanatheka bwanji kuti munthu ‘achite zinthu mosakhulupirika mwa kuchimwira zinthu zopatulika za Yehova mosadziwa’? (it-1 1130 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 4:27–5:4 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 81

  • Tachita Upainiya Limodzi kwa Zaka 60 Mothandizidwa ndi Yehova: (15 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi Takako ndi Hisako asangalala ndi zinthu zotani pochita upainiya? Kodi Takako anali ndi matenda otani, nanga n’chiyani chinamuthandiza? Kodi n’chiyani chawathandiza alongowa kukhala osangalala? Kodi chitsanzo chawo chikupereka bwanji umboni wa mfundo zopezeka m’malemba awa: Miyambo 25:11; Mlaliki 12:1; Aheberi 6:10?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 109

  • Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero