Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

November 23-29

LEVITIKO 6-7

November 23-29

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Nsembe Yosonyeza Kuyamikira”: (10 min.)

    • Le 7:11, 12​—Anthu ankapereka nsembe ina yachiyanjano mwa kufuna kwawo posonyeza kuyamikira (w19.11 22 ¶9)

    • Le 7:13-15​—Zinali ngati munthu amene akupereka nsembe yachiyanjanoyo komanso banja lake akudyera limodzi ndi Yehova posonyeza kuti ali naye pa mtendere (w00 8/15 15 ¶15)

    • Le 7:20​—Anthu oyera okha ndi amene akanatha kupereka nsembe yachiyanjano yovomerezeka (w00 8/15 19 ¶8)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 6:13​—Kodi Ayuda amakhulupirira kuti moto wapaguwa lansembe unayatsidwa bwanji, nanga Malemba amasonyeza chiyani? (it-1 833 ¶1)

    • Le 6:25​—Kodi nsembe zamachimo zinkasiyana bwanji ndi nsembe zopsereza komanso zachiyanjano? (si 27 ¶15)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 6:1-18 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 18

  • Khalani Bwenzi la Yehova​Uzithokoza:  (5 min.) Onerani vidiyoyi. Pemphani ana amene mwawasankhiratu, ngati n’zotheka, kuti abwere kupulatifomu kudzayankha mafunso okhudza vidiyoyo.

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 110

  • Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 30 ndi Pemphero