Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

November 30–December 6

LEVITIKO 8-9

November 30–December 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Umboni Wakuti Yehova Ankawadalitsa”: (10 min.)

    • Le 8:6-9, 12​—Mose analonga anthu unsembe (it-1 1207)

    • Le 9:1-5​—Mtundu wonse wa Aisiraeli unkaona pamene ansembe ankapereka nsembe zanyama zoyambirira (it-1 1208 ¶8)

    • Le 9:23, 24​—Yehova anasonyeza kuti anavomereza ansembewo (w19.11 23 ¶13)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 8:6​—Kodi tingaphunzire chiyani pa lamulo lakuti ansembe a ku Isiraeli ankafunika kukhala aukhondo? (w14 11/15 9 ¶6)

    • Le 8:14-17​—Pamene ankakhazikitsa unsembe, n’chifukwa chiyani Mose ndi amene anapereka nsembe osati Aroni? (it-2 437 ¶3)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 8:31–9:7 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU