November 9-15
LEVITIKO 1-3
Nyimbo Na. 20 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Chifukwa Chake Nsembe Zinkaperekedwa”: (10 min.)
[Onerani Vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Levitiko.]
Le 1:3; 2:1, 12—Chifukwa chake nsembe zopsereza komanso zambewu zinkaperekedwa (it-2 525; 528 ¶4)
Le 3:1—Chifukwa chake nsembe zachiyanjano zinkaperekedwa (it-2 526 ¶1)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Le 2:13—N’chifukwa chiyani ankayenera kuperekanso mchere popereka nsembe iliyonse? (Eze 43:24; w04 5/15 22 ¶2)
Le 3:17—N’chifukwa chiyani Aisiraeli sankaloledwa kudya mafuta, nanga tikuphunzirapo chiyani? (it-1 813; w04 5/15 22 ¶3)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 1:1-17 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani Yokambirana. Onerani vidiyoyi koma muziimitsa nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime ndipo funsani omvera mafunso omwe ali m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 2)
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“‘Timakobidi Tiwiri Tating’ono’ Tamtengo Wapatali”: (15 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi mkulu. Onerani vidiyo yakuti ‘Muzipereka Mphatso kwa Yehova’. Werengani kalata yochokera kunthambi yothokoza zopereka zimene yalandira m’chaka cha utumiki chapitachi.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 108
Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero