December 20-26
OWERUZA 10-12
Nyimbo Na. 127 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yefita Anali Munthu Wauzimu”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Owe 11:1—Kodi timadziwa bwanji kuti Yefita sanali mwana wapathengo? (it-2 26)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Owe 10:1-18 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani chitsanzo cha ulendo woyamba pogwiritsa ntchito kapepala kakuti Kodi Baibulo Mumalikhulupirira? (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 4)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 02 mfundo 5 (th phunziro 3)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Anadzipereka Kuyambira Ali Wamng’ono: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi vidiyoyi yakuphunzitsani chiyani pa nkhani ya kufunika kophunzitsa anthu ena? kufunika kodzipereka kwa Yehova udakali wamng’ono? kufunika kodzipereka kuti gulu la Yehova likugwiritse ntchito?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 9 ndime 9-21
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 122 ndi Pemphero