December 6-12
OWERUZA 6-7
Nyimbo Na. 38 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Pita ndi Mphamvu Zimene Ndakupatsazi”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Owe 6:27—Kodi chitsanzo cha Gidiyoni chingatithandize bwanji mu utumiki? (w05 1/15 26 ¶6)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Owe 6:1-16 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Baibulo—Aro 15:4. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 6)
Ulendo Woyamba: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo musonyezeni mmene angapezere kabukuka pa chipangizo chamakono. (th phunziro 15)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Ntchito Yovuta Yomwe Inatheka Ndi Mzimu Woyera”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kupanga Vidiyo ya “The New World Society in Action”.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 8 ndime 19-26, mfundo za m’Baibulo tsa. 114-117
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero