November 15-21
YOSWA 23-24
Nyimbo Na. 50 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mawu Omaliza Amene Yoswa Analimbikitsa Nawo Mtundu wa Aisiraeli”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yos 24:2—Kodi Tera yemwe anali bambo ake a Abulahamu ankalambira mafano? (w04 12/1 12 ¶1)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 24:19-33 (th phunziro 11)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 2)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 20)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 01 zomwe taphunzira, kubwereza, komanso zolinga (th phunziro 3)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Muzipewa Kugwirizana ndi Anthu a Makhalidwe Oipa Kuntchito: (7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzipewa Zinthu Zimene Zingawononge Khalidwe Lanu la Kukhulupirika—Kugwirizana ndi Anthu a Makhalidwe Oipa. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi kuchita zinthu ndi anthu a makhalidwe oipa kuntchito kunakhudza bwanji mlongoyu? Kodi anasintha chiyani, nanga zinamuthandiza bwanji? Kodi vidiyoyi yakuphunzitsani chiyani pankhani yopewa kugwirizana ndi anthu a makhalidwe oipa?
Mukhoza Kupeza Mabwenzi Kulikonse: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi ndi mavuto ati amene anachititsa kuti Akil ayambe kugwirizana ndi anyamata a makhalidwe oipa kusukulu? Kodi anapeza bwanji anzake abwino mumpingo? Kodi vidiyoyi yakuphunzitsani chiyani pa nkhani yopeza anzanu abwino?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 7 ndime 20-28, mfundo za m’Baibulo tsa. 100-103
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 67 ndi Pemphero