Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

Zimene Tinganene

Zimene Tinganene

Ulendo Woyamba mu November (Ntchito Yapadera)

Funso: Kodi zachiwawa komanso nkhondo zidzathadi?

Lemba: Sl 37:10, 11

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi ndi lonjezo la m’Baibulo liti lomwe limatipatsa chiyembekezo?

LEMBALI LIKUPEZEKA MU:

Ulendo Woyamba mu December *

Funso: Kodi Baibulo mumalikhulupirira?

Lemba: Aro 15:4

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi ndi lonjezo la m’Baibulo liti lomwe limatipatsa chiyembekezo?

LEMBALI LIKUPEZEKA MU:

Ulendo Wobwereza *

Funso: Kodi ndi lonjezo la m’Baibulo liti lomwe limatipatsa chiyembekezo?

Lemba: Chv 21:3, 4

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tingatani kuti tizimvetsa bwino Baibulo?

LEMBALI LIKUPEZEKA MU:

^ ndime 9 ^ ndime 15 Mukhoza kusintha funso komanso funso la ulendo wotsatira mogwirizana ndi mmene zinthu zilili kwanuko.