December 12-18
2 MAFUMU 16-17
Nyimbo Na. 115 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kuleza Mtima kwa Yehova Kuli ndi Malire”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mf 17:29—Kodi “Asamariya” otchulidwa pa lembali anali ndani, nanga dzinali linkaimira ndani patapita nthawi? (it-2 847)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 17:18-28 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene muli chitsanzo cha ulendo woyamba. Mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 4)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene muli chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 20)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 08 mfundo 5 (th phunziro 9)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muziyembekezera Mapeto a Dzikoli Molimba Mtima”: (5 min.) Nkhani yokambirana.
Zimene Gulu Lathu Lachita: (10 min.) Onerani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 31
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 74 ndi Pemphero