December 26–January 1
2 MAFUMU 20–21
Nyimbo Na. 41 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Pemphero Linachititsa Yehova Kuchitapo Kanthu”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mf 21:13—Kodi Yehova anayeza Yerusalemu ndi thabwa lowongolera m’njira yotani? (it-2 240 ¶1)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 21:1-15 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 4)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 6)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 08 mfundo 6 (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Mapemphero Athu ndi Amtengo Wapatali kwa Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ndimakonda Kupemphera.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 32 mfundo 5-6, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 142 ndi Pemphero