December 5-11
2 MAFUMU 13-15
Nyimbo Na. 127 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kuchita Zinthu Ndi Mtima Wonse Kumabweretsa Madalitso Ambiri”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mf 13:20, 21—Kodi chozizwitsa cha pa lembali chimasonyeza kuti kulambira zinthu zakale zopatulika sikulakwa? (w05 8/1 11 ¶3)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 13:20–14:7 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (2 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambitsani phunziro la Baibulo pogwiritsa ntchito phunziro 01 la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 20)
Nkhani: (5 min.) km 8/03 1—Mutu: Ntchito Imene Imatsitsimula. (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Yehova Sangaiwale Khama Limene Tinachita Pomutumikira”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Yehova Saiwala.
Zofunika Pampingo: (5 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 30
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 151 ndi Pemphero