November 21-27
2 MAFUMU 9-10
Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Anachita Zinthu Molimba Mtima, Modzipereka Komanso Mofunitsitsa”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mf 10:29, 31—Kodi tingaphunzire chiyani kuchokera pa zimene Yehu analakwitsa? (w11 11/15 5 ¶6-7)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 9:1-14 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu kwaulere, kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 12)
Nkhani: (5 min.) w13 5/15 8-9 ¶3-6—Mutu: Tsanzirani Yehova ndi Yesu pa Nkhani ya Kudzipereka. (th phunziro 16)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zimene Achinyamata Anzanu Amanena—Kuzengereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi n’chiyani chingachititse munthu kuchita zinthu mozengereza? N’chifukwa chiyani timasangalala tikakhala kuti sitinachite zinthu mozengereza?
“Zimene Zingatithandize Kuti Tisamazengereze Pochita Zinthu”: (10 min.) Nkhani yokambirana.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 28
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 19 ndi Pemphero