Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anachita Zinthu Molimba Mtima, Modzipereka Komanso Mofunitsitsa

Anachita Zinthu Molimba Mtima, Modzipereka Komanso Mofunitsitsa

Yehova anatuma Yehu kuti akaphe anthu onse a m’nyumba ya Mfumu Ahabu yemwe anali woipa (2Mf 9:6, 7w11 11/15 3 ¶2)

Yehu anachita zinthu mwamsanga popha Mfumu Yehoramu (mwana wa Ahabu) komanso Mfumukazi Yezebeli (yemwe anali mkazi wa Ahabu) (2Mf 9:22-24, 30-33; w11 11/15 4 ¶2-3; onani bokosi lakuti “‘Nyumba Yonse ya Ahabu Ifafanizidwe’​—2Mf 9:8”)

Yehu anachita zonse zimene Yehova anamuuza ndipo anasonyeza kuti anali wolimba mtima, wodzipereka komanso wofunitsitsa (2Mf 10:17; w11 11/15 5 ¶3-4)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndingatsanzire bwanji Yehu posonyeza kumvera lamulo lopezeka pa Mateyu 28:19, 20?’