November 7-13
2 MAFUMU 5-6
Nyimbo Na. 55 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tili Ndi Ambiri Kuposa Amene Ali Ndi Iwowo”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
2Mf 5:15, 16—N’chifukwa chiyani Elisa anakana mphatso ya Namani? (w05 8/1 9 ¶2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 5:1-14 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Uthenga Wabwino—Sl 37:10, 11. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 08 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 15)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Khalani Opatsa”: (15 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi mkulu. Onerani vidiyo yakuti Tikukuthokozani Chifukwa cha Mtima Wanu Wopatsa. Ayamikireni abale ndi alongo chifukwa cha zinthu zosiyanasiyana zimene amachita zosonyeza kuti ali ndi mtima wopatsa.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 26
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 30 ndi Pemphero