Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Elisa akuuza mtumiki wake kuti: “Ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi iwowo.”​—2Mf 6:16

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Tili Ndi Ambiri Kuposa Amene Ali Ndi Iwowo”

“Tili Ndi Ambiri Kuposa Amene Ali Ndi Iwowo”

Elisa ndi mtumiki wake anazunguliridwa ndi adani (2Mf 6:13, 14; it-1 716 ¶4)

Elisa sanachite mantha ndipo analimbikitsa mtumiki wake (2Mf 6:15-17; w13 8/15 30 ¶2; onani chithunzi chapachikuto)

Yehova anapulumutsa Elisa ndi mtumiki wake modabwitsa (2Mf 6:18, 19, it-1 343 ¶1)

Adani athu alibe mphamvu tikawayerekezera ndi Yehova. Zikanakhala zotheka kuti tione kumwamba, n‘kuona mmene Yehova akugwiritsira ntchito angelo poteteza anthu ake, kodi mukuganiza kuti tikanaona zotani?