Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

December 2-8

MASALIMO 113-118

December 2-8

Nyimbo Na. 127 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. Kodi Yehova Tidzamubwezera Chiyani?

(10 min.)

Yehova amatiteteza, amachita nafe zinthu mokoma mtima komanso amatipulumutsa (Sl 116:6-8; w01 1/1 11 ¶13)

Tingabwezere Yehova ngati pa moyo wathu timatsatira mfundo zake komanso malamulo ake (Sl 116:12, 14; w09 7/15 29 ¶4-5)

Tingabwezere Yehova popereka “nsembe zoyamikira” (Sl 116:17; w19.11 22-23 ¶9-11)

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 116:15—Kodi anthu a Mulungu “okhulupirika” amene akutchulidwa mu vesili ndi ndani? (w12 5/15 22 ¶1-3)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Kulangiza Molimba Mtima—Zomwe Yesu Anachita

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 12 mfundo 1-2.

5. Kulangiza Molimba Mtima—Zomwe Mungachite Potsanzira Yesu

(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 12 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 60

6. Zofunika Pampingo

(15 min.)

7. Phunziro la Baibulo la Mpingo

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero