December 9-15
SALIMO 119:1-56
Nyimbo Na. 124 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. “Kodi Wachinyamata Angakhale Bwanji Woyera pa Moyo Wake?”
(10 min.)
Akamadzifufuza nthawi zonse (Sl 119:9; w87 11/1 18 ¶10)
Akamatsatira zikumbutso za Mulungu (Sl 119:24, 31, 36; w06 6/15 25 ¶1)
Akamapewa kuyang’ana zinthu zopanda pake (Sl 119:37; w10 4/15 20 ¶2)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ndamva zikumbutso ziti zimene zingandithandize kukhalabe ndi makhalidwe abwino?’
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Sl 119—Kodi Salimoli linalembedwa m’njira yotani, nanga n’kutheka kuti analilemba choncho chifukwa chiyani? (w05 4/15 10 ¶2)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Sl 119:1-32 (th phunziro 5)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Yambani kukambirana ndi munthu amene mwakumana naye mumsewu pamene mukulalikira ulaliki wa kunyumba ndi nyumba. (lmd phunziro 1 mfundo 4)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Pa ulendo wapita, mwininyumbayo anakuuzani kuti wachibale wake kapena mnzake wamwalira. (lmd phunziro 9 mfundo 3)
6. Nkhani
(5 min.) ijwyp 83—Mutu: Kodi Ndingatani Kuti Ndisamagonje Poyesedwa? (th phunziro 20)
Nyimbo Na. 40
7. Vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya December
(10 min.) Onerani VIDIYOYI.
8. Zofunika Pampingo
(5 min.)
9. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 19 ¶6-13