November 11-17
SALIMO 106
Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. “Iwo Anaiwala Mulungu, Mpulumutsi Wawo”
(10 min.)
Aisiraeli atayamba kuchita mantha, anapandukira Yehova (Eks 14:11, 12; Sl 106:7-9)
Aisiraeli atamva njala komanso ludzu, anayamba kung’ung’udzira Yehova (Eks 15:24; 16:3, 8; 17:2, 3; Sl 106:13, 14)
Pamene Aisiraeli anali ndi nkhawa, anayamba kulambira mafano (Eks 32:1; Sl 106:19-21; w18.07 20 ¶13)
FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi kuganizira mmene Yehova wakhala akutithandizira m’mbuyomu, kungatithandize bwanji pamene takumana ndi mavuto?
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Sl 106:36, 37—Kodi pali kugwirizana kotani pakati pa kulambira mafano ndi kupereka nsembe kwa ziwanda? (w06 7/15 13 ¶9)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Sl 106:21-48 (th phunziro 10)
4. Kuphunzitsa M’njira Yosavuta—Zomwe Yesu Anachita
(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 11 mfundo 1-2.
5. Kuphunzitsa M’njira Yosavuta—Zomwe Mungachite Potsanzira Yesu
(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 11 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”
Nyimbo Na. 78
6. Zofunika Pampingo
(15 min.)
7. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 18 ¶1-5, bokosi patsamba 142, 144