October 17-23
MIYAMBO 12-16
Nyimbo Na. 69 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Nzeru Ndi Yabwino Kuposa Golide”: (10 min.)
Miy. 16:16, 17—Munthu wanzeru amaphunzira Mawu a Mulungu komanso kuwagwiritsa ntchito (w07 7/15 8)
Miy. 16:18, 19—Munthu wanzeru amapewa kunyada ndiponso kudzikuza (w07 7/15 8-9)
Miy. 16:20-24—Munthu wanzeru amalankhula zinthu zothandiza ena (w07 7/15 9-10)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Miy. 15:15—Kodi tingatani kuti tizisangalala kwambiri pa moyo wathu? (g 11/13 16)
Miy. 16:4—Kodi Yehova angagwiritse ntchito bwanji anthu oipa kuti akwaniritse zolinga zake? (w07 5/15 18-19)
Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Miy. 15:18-33; 16:1-6
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yoh. 11:11-14—Kuphunzitsa Choonadi. Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Gen. 3:1-6; Aroma 5:12—Kuphunzitsa Choonadi. Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 202 ndime 18-19—Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 117
“Zimene Tingachite Kuti Ndemanga Zathu Zizikhala Zabwino”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Poyamba, onetsani vidiyo yakuti, Khalani Bwenzi la Yehova—Uzikonzekera Zimene Ukayankhe. Kenako pemphani ana amene munawasankhiratu kuti abwere kupulatifomu ndipo muwafunse mafunso awa: Kodi muyenera kuchita zinthu 4 ziti pokonzekera ndemanga? N’chifukwa chiyani tingakhalebe osangalala ngakhale kuti sitinapatsidwe mwayi woyankha pamisonkhano?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 9 ndime 1-13
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero