October 24-30
MIYAMBO 17-21
Nyimbo Na. 76 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yesetsani Kukhala Mwamtendere ndi Ena”: (10 min.)
Miy. 19:11—Muzikhala odekha munthu wina akakukhumudwitsani (w14 12/1 12-13)
Miy. 18:13, 17; 21:13—Muzitsimikizira kuti mukudziwa nkhani yonse (w11 8/15 30 ndime 11-14)
Miy. 17:9—Muzisonyeza chikondi pokhululukira munthu amene wakulakwirani (w11 8/15 31 ndime 17)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Miy. 17:5—Fotokozani chifukwa chimodzi chimene tiyenera kusankhira zosangalatsa mwanzeru. (w10 11/15 6 ndime 17; w10 11/15 31 ndime 15)
Miy. 20:25—Kodi mfundo ya pa lembali ingathandize bwanji anthu amene akufuna kukhala pa chibwenzi komanso kulowa m’banja? (w09 5/15 15-16 ndime 12-13)
Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Miy. 18:14-24; 19:1-10
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) M’patseni munthuyo kapepala koitanira anthu kumisonkhano. (inv)
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) inv—Pomaliza, muuzeni kuti mukufuna kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 57 ndime 14-15—Thandizani munthuyo kuona kuti ayenera kusintha mmene amavalira akamapita kumisonkhano.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 77
Kukhazikitsa Mtendere Kumabweretsa Madalitso: (15 min.) Nkhani yokambirana. Poyamba, onetsani vidiyo yakuti Kukhazikitsa Mtendere Kumabweretsa Madalitso. Kenako funsani mafunso awa: Kodi tiyenera kupewa zinthu ziti tikasemphana maganizo ndi munthu wina? Kodi timapeza madalitso ati tikamatsatira mfundo za pa Miyambo 17:9 ndi Mateyu 5:23, 24?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 9 ndime 14-24 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 82.
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 144 ndi Pemphero