Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

October 1-​7

YOHANE 9-10

October 1-​7

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yesu Amasamalira Nkhosa Zake”: (10 min.)

    • Yoh. 10:1-3, 11, 14​—Yesu yemwe ndi “m’busa wabwino,” amadziwa nkhosa zake ndipo amazisamalira bwino kwambiri (“Khola la nkhosa” zithunzi ndi mavidiyo pa Yoh. 10:1, nwtsty; w11 5/15 7-8 ¶5)

    • Yoh. 10:4, 5​—Nkhosa zimadziwa mawu a Yesu osati mawu a alendo (cf 125 ¶17)

    • Yoh. 10:16​—Nkhosa za Yesu zimakhala zogwirizana (“kuzibweretsa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 10:16, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yoh. 9:38​—Kodi zimene munthu yemwe poyamba anali wakhungu anachita pogwadira Yesu zinkatanthauza chiyani? (“anamugwadira” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 9:38, nwtsty)

    • Yoh. 10:22​—Kodi chikondwerero chopereka kachisi kwa Mulungu chinali chiyani? (“chikondwerero cha kupereka kachisi kwa Mulungu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 10:22, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 9:1-17

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 62

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 7

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 10 ndi Pemphero