Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 13-14

“Ndakupatsani Chitsanzo”

“Ndakupatsani Chitsanzo”

13:5, 12-15

Pamene Yesu anasambitsa mapazi a ophunzira ake, anawaphunzitsa kuti akhale odzichepetsa komanso azigwira ntchito zooneka zotsika pothandiza abale awo.

Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndine wodzichepetsa . . .

  • ndikasemphana maganizo ndi anthu ena?

  • ena akandipatsa malangizo?

  • ndikamagwira nawo ntchito yosamalira kapena kukonza Nyumba ya Ufumu?