Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

October 29–​November 4

YOHANE 18-19

October 29–​November 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yesu Anachitira Umboni Choonadi”: (10 min.)

    • Yoh. 18:36​—Choonadi chimafotokoza kwambiri za Ufumu wa Mesiya

    • Yoh. 18:37​—Yesu anachitira umboni choonadi chokhudza zolinga za Mulungu (“kudzachitira umboni,” “choonadi” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 18:37, nwtsty)

    • Yoh. 18:38a​—Pilato anatsutsa mfundo yoti padzikoli pangapezeke choonadi (“Choonadi n’chiyani?” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 18:38a, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yoh. 19:30​—Kodi mawu akuti Yesu ‘anapereka mzimu wake’ amatanthauza chiyani? (“kupereka mzimu wake” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 19:30, nwtsty)

    • Yoh. 19:31​—Kodi pali umboni wotani womwe umasonyeza kuti Yesu anaphedwa pa Nisani 14 mu 33 C.E? (“Sabata la tsiku limeneli linali lalikulu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 19:31, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 18:1-14

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. Kenako musonyezeni webusaiti yathu ya jw.org.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse komanso funso limene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 14 ¶6-7

MOYO WATHU WACHIKHRISTU