Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 18-19

Yesu Anachitira Umboni Choonadi

Yesu Anachitira Umboni Choonadi

18:36-38a

Yesu anachitira umboni choonadi chokhudza zolinga za Mulungu

  • M’MAWU: Iye ankalalikira mwakhama choonadi chonena za Ufumu wa Mulungu

  • M’ZOCHITA: Zimene anachita pa moyo wake zinasonyeza kuti maulosi a m’Baibulo ndi olondola

Nafenso monga otsatira a Yesu, timachitira umboni choonadi

  • M’MAWU: Ngakhale ena azitinyoza, timalalikira mwakhama uthenga wabwino wonena za Ufumu wa Mulungu womwe Mfumu yake ndi Yesu Khristu

  • M’ZOCHITA: Timasonyeza kuti tili ku mbali ya ulamuliro wa Yesu tikamachita zimene Mulungu amafuna komanso tikamapewa kukhala mbali ya dziko