October 19-25
EKISODO 35-36
Nyimbo Na. 92 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Anathandizidwa Kugwira Ntchito ya Yehova”: (10 min.)
Eks 35:25, 26—Yehova anadalitsa mtima wofunitsitsa wa anthu ake (w14 12/15 4 ¶4)
Eks 35:30-35—Mzimu woyera unathandiza Bezaleli ndi Oholiabu kuti azigwira “ntchito ina iliyonse” (w11 12/15 19 ¶6)
Eks 36:1, 2—Yehova anali woyenera kulandira ulemerero chifukwa cha ntchito imene anthuwa anagwira (w11 12/15 19 ¶7)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Eks 35:1-3—Kodi tikuphunzira chiyani pa lamulo la Sabata? (w05 5/15 23 ¶14)
Eks 35:21—Kodi tingatsanzire bwanji mtima wopatsa wa Aisiraeli? (w00 11/1 29 ¶1)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Eks 35:1-24 (th phunziro 11)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 11)
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako musonyezeni webusaiti yathu n’kumupatsa khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 4)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) bhs 26 ¶18-20 (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Lipoti la Komiti Yoona za Ntchito Yofalitsa Mabuku la 2018: (15 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso awa: Kodi gulu lasintha zinthu ziti zokhudza kusindikiza mabuku, nanga n’chifukwa chiyani? Kodi kuchepetsa mabuku amene amasindikizidwa kwathandiza pa ntchito ina iti? Kodi ntchito yomasulira mabuku ndi yofunika bwanji pa kupereka chakudya chauzimu? Kodi tapeza madalitso otani chifukwa cha mavidiyo komanso kukhala ndi mabuku pa zipangizo?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 105
Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero