October 26–November 1
EKISODO 37-38
Nyimbo Na. 43 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Maguwa Ansembe a Chihema Anali Ofunika pa Kulambira Koona”: (10 min.)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Eks 37:1, 10, 25—N’chifukwa chiyani mtengo wa mthethe unali wabwino kupangira chihema? (it-1 36)
Eks 38:8—Kodi magalasi odziyang’anira akale ankasiyana bwanji ndi amasiku ano? (w15 4/1 15 ¶4)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Eks 37:1-24 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako gawirani magazini yaposachedwapa imene ili ndi nkhani yomwe mwininyumba anayambitsa. (th phunziro 12)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) bhs 199 ¶8-9 (th phunziro 7)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (5 min.)
“Tidzagwira Ntchito Yapadera mu November Yolengeza za Ufumu wa Mulungu”: (10 min.) Nkhani Yokambirana. Onerani ndi kukambirana vidiyo ya ulendo woyamba ya November.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 106
Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 16 ndi Pemphero