Akulalikira mwamwayi ku South Korea

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU September 2018

Zimene Tinganene

Zitsanzo za zimene tinganene zokhudza mmene Mulungu amaonera anthu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Chozizwitsa Choyamba cha Yesu

Chozizwitsa choyamba chimene Yesu anachita chimatithandiza kumudziwa bwino.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yesu Analalikira Mayi Wachisamariya

Pamene ankalalikira mayi wachisamariya, Yesu anayamba ndi chitsanzo cha zimene mayiyo ankachita tsiku ndi tsiku.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Mmene Mungayambire Kucheza ndi Anthu Kuti Muwalalikire Mwamwayi

Kodi mungawonjezere bwanji luso lanu pa nkhani yoyamba kucheza ndi anthu kuti muwalalikire?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzitsatira Yesu Muli ndi Zolinga Zabwino

Ophunzira ena anakhumudwa ndipo anasiya kutsatira Yesu chifukwa zolinga zawo zinali zadyera.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Sipanawonongeke Chilichonse

Mofanana ndi Yesu ifenso tingasonyeza kuyamikira zimene Yehova amatipatsa, popewa kuwononga zinthu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yesu Ankalemekeza Atate Wake

Cholinga chachikulu chimene Yesu anali nacho chinali kukwaniritsa ntchito imene Yehova anamupatsa.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzitsanzira Khristu pa Nkhani Yokhala Odzichepetsa Komanso Kuzindikira Malire Anu

Kodi tingatsanzire bwanji Yesu tikapatsidwa udindo kapena utumiki winawake mumpingo?