Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

September 10-16

YOHANE 3-4

September 10-16

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yesu Analalikira Mayi Wachisamariya”: (10 min.)

    • Yoh. 4:6, 7​—Ngakhale kuti anali atatopa, Yesu anayamba kulankhula ndi mayi wachisamariya (“atatopa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 4:6, nwtsty)

    • Yoh. 4:21-24​—Zimene Yesu anachitazi zinachititsa kuti anthu ambiri amve uthenga wabwino

    • Yoh. 4:39-41​—Chifukwa cha khama limene Yesu anachita, Asamariya ambiri anayamba kumukhulupirira

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yoh. 3:29​—Kodi vesi limeneli likutanthauza chiyani? (“mnzake wa mkwati” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 3:29, nwtsty)

    • Yoh. 4:10​—Kodi n’kutheka kuti mayi wachisamariyayu ankaganiza chiyani pamene Yesu ananena za “madzi amoyo,” koma kodi Yesu ankatanthauza chiyani kwenikweni? (“madzi amoyo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 4:10, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 4:1-15

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU