Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

September 24-30

YOHANE 7-8

September 24-30

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yesu Ankalemekeza Atate Wake”: (10 min.)

    • Yoh. 7:15-18​—Anthu ena atamuyamikira kuti amaphunzitsa bwino, Yesu anawauza kuti zimene amaphunzitsazo zimachokera kwa Yehova (cf 100-101 ¶5-6)

    • Yoh. 7:28, 29​—Yesu ananena kuti anachita kutumidwa ndi Yehova, zomwe zikusonyeza kuti amamumvera

    • Yoh. 8:29​—Yesu anauza anthu kuti iye amachita zinthu zimene zimakondweretsa Yehova nthawi zonse (w11 3/15 11 ¶19)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yoh. 7:8-10​—Kodi pamenepa Yesu ankawanamiza abale akewo? (w07 2/1 6 ¶4)

    • Yoh. 8:58​—Kodi n’chiyani chikutitsimikizira kuti mawu amene ali kumapeto kwa vesili akuti “ine n’kuti ndilipo kale” ndi olondola, nanga n’chifukwa chiyani kudziwa zimenezi n’kofunika? (“ine n’kuti ndilipo kale” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 8:58, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 8:31-47

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. Kenako muitanireni kumisonkhano yathu.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse ndipo gawirani buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lvs 9-10 ¶10-11

MOYO WATHU WACHIKHRISTU