September 3-9
YOHANE 1-2
Nyimbo Na. 13 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Chozizwitsa Choyamba cha Yesu”: (10 min.)
[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yohane.]
Yoh. 2:1-3—Pa mwambo wina wa ukwati panachitika zinthu zomwe zikanachititsa manyazi banja latsopanolo (w15 6/15 4 ¶3)
Yoh. 2:4-11—Zimene Yesu anachita zinalimbitsa chikhulupiriro cha ophunzira ake (jy 41 ¶6)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Yoh. 1:1—Kodi n’chiyani chikusonyeza kuti Yohane sankatanthauza kuti “Mawu” anali Mulungu Wamphamvuyonse? (“Mawu” “ndi” “Mawuyo anali mulungu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 1:1, nwtsty)
Yoh. 1:29—N’chifukwa chiyani Yohane M’batizi anatchula Yesu kuti “Mwanawankhosa wa Mulungu”? (“Mwanawankhosa wa Mulungu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 1:29, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 1:1-18
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha wobwereza woyamba.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs tsamba 50, Mfundo 2
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (8 min.)
Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya September.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 3
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero